-
Nehemiya 3:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Yedaya mwana wa Harumafi anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba yake kuchokera pamene Refaya analekezera. Kenako Hatusi mwana wa Hasabineya anapitiriza kuchokera pamene Yedaya analekezera.
-