Nehemiya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Yedaya mwana wamwamuna wa Harumafi anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba yake+ kuchokera pamene Refaya analekezera. Kenako Hatusi mwana wamwamuna wa Hasabineya anakonza mpandawo kuchokera pamene Yedaya analekezera.
10 Ndiyeno Yedaya mwana wamwamuna wa Harumafi anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba yake+ kuchokera pamene Refaya analekezera. Kenako Hatusi mwana wamwamuna wa Hasabineya anakonza mpandawo kuchokera pamene Yedaya analekezera.