-
Nehemiya 3:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kenako Salumu mwana wa Halohesi, kalonga wa hafu ya chigawo cha Yerusalemu, anapitiriza kukonza mpandawo limodzi ndi ana ake aakazi kuchokera pamene enawo anasiyira.
-