Nehemiya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Salumu mwana wamwamuna wa Halohesi, kalonga+ wa hafu ya chigawo cha Yerusalemu, anakonza mpandawo pamodzi ndi ana ake aakazi kuchokera pamene winayo analekezera. Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:12 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2019, tsa. 23
12 Kenako Salumu mwana wamwamuna wa Halohesi, kalonga+ wa hafu ya chigawo cha Yerusalemu, anakonza mpandawo pamodzi ndi ana ake aakazi kuchokera pamene winayo analekezera.