Nehemiya 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Baruki mwana wa Zabai,+ anagwira ntchito mwachangu kwambiri moti anakonza gawo lina la mpandawo, kuchokera pamene panali khoma lothandizira kuti mpanda usagwe kukafika pageti la nyumba ya Eliyasibu+ mkulu wa ansembe.
20 Baruki mwana wa Zabai,+ anagwira ntchito mwachangu kwambiri moti anakonza gawo lina la mpandawo, kuchokera pamene panali khoma lothandizira kuti mpanda usagwe kukafika pageti la nyumba ya Eliyasibu+ mkulu wa ansembe.