Nehemiya 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako, Baruki mwana wamwamuna wa Zabai,+ anagwira ntchito mwachangu kwambiri+ ndi kukonza gawo lina la mpandawo, kuchokera pa Mchirikizo wa Khoma kukafika pachipata cha nyumba ya Eliyasibu+ mkulu wa ansembe.
20 Kenako, Baruki mwana wamwamuna wa Zabai,+ anagwira ntchito mwachangu kwambiri+ ndi kukonza gawo lina la mpandawo, kuchokera pa Mchirikizo wa Khoma kukafika pachipata cha nyumba ya Eliyasibu+ mkulu wa ansembe.