Nehemiya 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Binui mwana wa Henadadi anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera panyumba ya Azariya kukafika pamene panali khoma lothandizira kuti mpanda usagwe+ mpaka pakona ya mpanda wa mzindawo.
24 Binui mwana wa Henadadi anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera panyumba ya Azariya kukafika pamene panali khoma lothandizira kuti mpanda usagwe+ mpaka pakona ya mpanda wa mzindawo.