Nehemiya 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zadoki+ mwana wa Imeri anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba yake. Semaya mwana wa Sekaniya, woyangʼanira Geti ya Kumʼmawa,+ anapitiriza kuchokera pamene Zadoki analekezera.
29 Zadoki+ mwana wa Imeri anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba yake. Semaya mwana wa Sekaniya, woyangʼanira Geti ya Kumʼmawa,+ anapitiriza kuchokera pamene Zadoki analekezera.