Nehemiya 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Osula golide ndi amalonda anakonza mpandawo kuyambira pachipinda chapadenga chapakona kukafika pa Geti la Nkhosa.+
32 Osula golide ndi amalonda anakonza mpandawo kuyambira pachipinda chapadenga chapakona kukafika pa Geti la Nkhosa.+