Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Eliyasibu+ mkulu wa ansembe ndi abale ake, ansembe, anayamba kumanga Geti la Nkhosa+ ndipo analiyeretsa+ nʼkuika zitseko zake. Anayeretsa chigawo chonse mpaka ku Nsanja ya Meya+ nʼkukafika ku Nsanja ya Hananeli.+

  • Yohane 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ku Yerusalemu pa Geti la Nkhosa+ pali damu limene mʼChiheberi limatchedwa Betizata. Mʼmbali mwa damulo muli makonde 5 amene ali ndi zipilala.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena