Nehemiya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chonde, lero abwezereni minda yawo+ ya tirigu, ya mpesa, ya maolivi, nyumba zawo ndiponso gawo limodzi pa magawo 100 a ndalama, tirigu, vinyo watsopano komanso mafuta zimene munawauza kuti azikupatsani ngati chiwongoladzanja.”
11 Chonde, lero abwezereni minda yawo+ ya tirigu, ya mpesa, ya maolivi, nyumba zawo ndiponso gawo limodzi pa magawo 100 a ndalama, tirigu, vinyo watsopano komanso mafuta zimene munawauza kuti azikupatsani ngati chiwongoladzanja.”