Nehemiya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chonde, lero abwezereni minda yawo ya tirigu,+ minda yawo ya mpesa, minda yawo ya maolivi, nyumba zawo ndi limodzi mwa magawo 100 a ndalama, tirigu, vinyo watsopano ndi mafuta zimene munalandira kwa iwo monga chiwongoladzanja.”
11 Chonde, lero abwezereni minda yawo ya tirigu,+ minda yawo ya mpesa, minda yawo ya maolivi, nyumba zawo ndi limodzi mwa magawo 100 a ndalama, tirigu, vinyo watsopano ndi mafuta zimene munalandira kwa iwo monga chiwongoladzanja.”