-
Nehemiya 5:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Atamva zimenezi anati: “Tiwabwezera ndipo sitiwauzanso kuti atipatse kenakake. Tichita ndendende mmene mwanenera.” Choncho ndinaitana ansembe nʼkulumbiritsa anthuwo kuti achite zimene alonjeza.
-