Nehemiya 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo iwo anati: “Tiwabwezera,+ ndipo sitiwaumirizanso kuti atipatse kena kalikonse.+ Tichita ndendende mmene wanenera.”+ Choncho ndinaitana ansembe ndi kulumbiritsa olakwawo kuti achite mogwirizana ndi mawu amenewa.+
12 Pamenepo iwo anati: “Tiwabwezera,+ ndipo sitiwaumirizanso kuti atipatse kena kalikonse.+ Tichita ndendende mmene wanenera.”+ Choncho ndinaitana ansembe ndi kulumbiritsa olakwawo kuti achite mogwirizana ndi mawu amenewa.+