-
Nehemiya 5:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndinauza anthu kuti tsiku lililonse azipha ngʼombe imodzi yamphongo, nkhosa zabwino kwambiri zokwana 6 ndiponso mbalame, ndipo pakatha masiku 10 tinkakhala ndi vinyo wambiri wamtundu uliwonse. Koma sindinapemphe kuti andipatse chakudya choyenera kuperekedwa kwa bwanamkubwa chifukwa anthuwa ankagwira kale ntchito yolemetsa.
-