-
Nehemiya 13:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Kenako ndinawachenjeza kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukugona kunja kwa mpanda? Mukachitanso zimenezi, ndidzachita kukuthamangitsani.” Kuyambira nthawi imeneyo sanabwerenso pa tsiku la Sabata.
-