Nehemiya 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo ndinawachenjeza+ kuti: “N’chifukwa chiyani mukugona kunja kwa mpanda? Mukachitanso zimenezi ndikukhaulitsani.”+ Kuyambira nthawi imeneyo sanabwerenso pa tsiku la sabata.
21 Pamenepo ndinawachenjeza+ kuti: “N’chifukwa chiyani mukugona kunja kwa mpanda? Mukachitanso zimenezi ndikukhaulitsani.”+ Kuyambira nthawi imeneyo sanabwerenso pa tsiku la sabata.