Yobu 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Pali malo amene anthu amakumba siliva,Ndiponso malo amene amakumba golide yemwe amamuyenga.+