Miyambo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Siliva amamuyengera mʼmbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera mungʼanjo,+Koma Yehova ndi amene amayesa mitima.+ Malaki 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye adzakhala pansi ngati woyenga zitsulo ndiponso ngati woyeretsa siliva.+ Adzayeretsa ana a Levi ndipo adzawayeretsa ngati golide ndi siliva. Akamadzapereka nsembe zawo ngati mphatso, Yehova adzaona kuti nsembe zawozo akuzipereka molungama.
3 Siliva amamuyengera mʼmbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera mungʼanjo,+Koma Yehova ndi amene amayesa mitima.+
3 Iye adzakhala pansi ngati woyenga zitsulo ndiponso ngati woyeretsa siliva.+ Adzayeretsa ana a Levi ndipo adzawayeretsa ngati golide ndi siliva. Akamadzapereka nsembe zawo ngati mphatso, Yehova adzaona kuti nsembe zawozo akuzipereka molungama.