Yobu 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Miyala yamtengo wapatali ya korali ndi kulusitalo sitingaiyerekezere nʼkomwe ndi nzeru.+Ndipo thumba lodzaza ndi nzeru ndi lamtengo wapatali kuposa thumba lodzaza ndi ngale. Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:18 Nsanja ya Olonda,4/1/1999, ptsa. 3-7
18 Miyala yamtengo wapatali ya korali ndi kulusitalo sitingaiyerekezere nʼkomwe ndi nzeru.+Ndipo thumba lodzaza ndi nzeru ndi lamtengo wapatali kuposa thumba lodzaza ndi ngale.