Yobu 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndinkanena kuti, ‘Ndidzafera mʼnyumba yanga,*+Ndipo masiku anga adzakhala ochuluka ngati mchenga.