Yobu 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nʼchifukwa chiyani mukumudandaula?+ Kodi nʼchifukwa chakuti sanakuyankheni mawu anu onse?+