Yobu 38:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndi ndani anaika nzeru mʼmitambo,*+Kapena ndi ndani anachititsa kuti zinthu zakuthambo zikhale zozindikira?*+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:36 Nsanja ya Olonda,11/1/1998, tsa. 32
36 Ndi ndani anaika nzeru mʼmitambo,*+Kapena ndi ndani anachititsa kuti zinthu zakuthambo zikhale zozindikira?*+