Salimo 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati munthu amaopa Yehova,+ Iye adzamulangiza njira imene akuyenera kusankha.+