Salimo 37:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pewani kuchita zoipa ndipo muzichita zabwino,+Mukatero mudzakhala padziko lapansi mpaka kalekale.