Salimo 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Siyani kuchita zinthu zoipa ndipo muzichita zabwino.+Yesetsani kukhala mwamtendere ndi ena komanso kuulimbikitsa.+ Yesaya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Phunzirani kuchita zabwino, muzichita chilungamo,+Dzudzulani munthu wopondereza ena,Tetezani ufulu wa mwana wamasiye,Ndipo muteteze mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+
14 Siyani kuchita zinthu zoipa ndipo muzichita zabwino.+Yesetsani kukhala mwamtendere ndi ena komanso kuulimbikitsa.+
17 Phunzirani kuchita zabwino, muzichita chilungamo,+Dzudzulani munthu wopondereza ena,Tetezani ufulu wa mwana wamasiye,Ndipo muteteze mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+