Salimo 51:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukatero mudzasangalala ndi nsembe zachilungamo,Mudzakondwera ndi nsembe zopsereza komanso nsembe zathunthu.Pamenepo ngʼombe zamphongo zidzaperekedwa paguwa lanu la nsembe.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:19 Nsanja ya Olonda,3/15/1993, tsa. 18
19 Mukatero mudzasangalala ndi nsembe zachilungamo,Mudzakondwera ndi nsembe zopsereza komanso nsembe zathunthu.Pamenepo ngʼombe zamphongo zidzaperekedwa paguwa lanu la nsembe.+