Salimo 52:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nʼchifukwa chake Mulungu adzakugwetsa ndipo sudzakhalakonso.+Adzakugwira nʼkukukokera kutali ndi tenti yako,+Ndipo adzakuzula nʼkukuchotsa mʼdziko la anthu amoyo.+ (Selah)
5 Nʼchifukwa chake Mulungu adzakugwetsa ndipo sudzakhalakonso.+Adzakugwira nʼkukukokera kutali ndi tenti yako,+Ndipo adzakuzula nʼkukuchotsa mʼdziko la anthu amoyo.+ (Selah)