Salimo 80:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Sonyezani mphamvu zanu+Pa Efuraimu, Benjamini ndi Manase.Bwerani mudzatipulumutse.+