Salimo 80:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munalambula malo odzalapo mtengo wa mpesawo,Ndipo unazika mizu nʼkudzaza dziko.+