Salimo 109:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakamwa panga padzatamanda Yehova ndi mtima wonse.Ndidzamutamanda pamaso pa anthu ambiri.+