Salimo 145:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ufumu wanu ndi ufumu wamuyaya,Ndipo ulamuliro wanu udzakhalapo ku mibadwo yonse.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 145:13 Nsanja ya Olonda,9/15/1990, ptsa. 17-18