Miyambo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa kupeza nzeru nʼkwabwino kuposa kupeza siliva,Ndipo kukhala nazo monga phindu nʼkwabwino kuposa kukhala ndi golide.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Nsanja ya Olonda,12/15/1993, tsa. 19 Galamukani!,5/8/1992, tsa. 32
14 Chifukwa kupeza nzeru nʼkwabwino kuposa kupeza siliva,Ndipo kukhala nazo monga phindu nʼkwabwino kuposa kukhala ndi golide.+