Miyambo 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chifukwa Yehova amanyansidwa ndi munthu wachiphamaso,+Koma anthu owongoka mtima amakhala nawo pa ubwenzi wolimba.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:32 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 8 Nsanja ya Olonda,7/15/1993, ptsa. 21-22
32 Chifukwa Yehova amanyansidwa ndi munthu wachiphamaso,+Koma anthu owongoka mtima amakhala nawo pa ubwenzi wolimba.+