Miyambo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sitingayembekezere kuti munthu wopusa alankhule zinthu zanzeru.*+ Ndipo nʼzosayenera kuti wolamulira* azilankhula zabodza.+
7 Sitingayembekezere kuti munthu wopusa alankhule zinthu zanzeru.*+ Ndipo nʼzosayenera kuti wolamulira* azilankhula zabodza.+