Miyambo 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Aliyense amene amauza munthu woipa kuti, “Ndiwe wolungama,”+ Anthu adzamutemberera ndipo mitundu ya anthu idzaitanira tsoka pa iye. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:24 Nsanja ya Olonda,11/1/1989, tsa. 5
24 Aliyense amene amauza munthu woipa kuti, “Ndiwe wolungama,”+ Anthu adzamutemberera ndipo mitundu ya anthu idzaitanira tsoka pa iye.