Mlaliki 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho ndinaganizira zinthu zonsezi mumtima mwanga ndipo ndinaona kuti anthu olungama, anthu anzeru limodzi ndi ntchito zawo ali mʼmanja mwa Mulungu woona.+ Anthu sakudziwa za chikondi kapena chidani chimene chinalipo iwo asanakhalepo.
9 Choncho ndinaganizira zinthu zonsezi mumtima mwanga ndipo ndinaona kuti anthu olungama, anthu anzeru limodzi ndi ntchito zawo ali mʼmanja mwa Mulungu woona.+ Anthu sakudziwa za chikondi kapena chidani chimene chinalipo iwo asanakhalepo.