Mlaliki 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chinthu chomvetsa chisoni chimene chimachitika padziko lapansi pano ndi ichi: Chifukwa chakuti mapeto a anthu onse ndi ofanana,+ mitima ya anthu ndi yodzaza ndi zoipa. Mumtima mwawo mumakhala misala pa nthawi imene ali ndi moyo ndipo kenako amafa.
3 Chinthu chomvetsa chisoni chimene chimachitika padziko lapansi pano ndi ichi: Chifukwa chakuti mapeto a anthu onse ndi ofanana,+ mitima ya anthu ndi yodzaza ndi zoipa. Mumtima mwawo mumakhala misala pa nthawi imene ali ndi moyo ndipo kenako amafa.