Nyimbo ya Solomo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wachikondi wanga ali ngati kathumba konunkhira ka mule* kwa ine.+Iye amakhala pakati pa mabere anga usiku wonse.
13 Wachikondi wanga ali ngati kathumba konunkhira ka mule* kwa ine.+Iye amakhala pakati pa mabere anga usiku wonse.