Yesaya 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu amene amakudalirani ndi mtima wonse* mudzawateteza.Mudzawapatsa mtendere wosatha,+Chifukwa amadalira inu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:3 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 181/15/1988, ptsa. 15-16 Yesaya 1, ptsa. 276-277
3 Anthu amene amakudalirani ndi mtima wonse* mudzawateteza.Mudzawapatsa mtendere wosatha,+Chifukwa amadalira inu.+