Yesaya 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe ukunena kuti, ‘Ine ndili ndi pulani komanso mphamvu zoti zindithandize pankhondo.’ Koma zimenezi nʼzabodza. Kodi ukudalira ndani kuti undipandukire?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:5 Yesaya 1, tsa. 386
5 Iwe ukunena kuti, ‘Ine ndili ndi pulani komanso mphamvu zoti zindithandize pankhondo.’ Koma zimenezi nʼzabodza. Kodi ukudalira ndani kuti undipandukire?+