Yesaya 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe wanena kuti (koma ndi mawu a pakamwa chabe), ‘Ine ndili ndi nzeru ndi mphamvu zofunika pankhondo.’+ Kodi ukudalira ndani popandukira ine?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:5 Yesaya 1, tsa. 386
5 Iwe wanena kuti (koma ndi mawu a pakamwa chabe), ‘Ine ndili ndi nzeru ndi mphamvu zofunika pankhondo.’+ Kodi ukudalira ndani popandukira ine?+