Yesaya 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ubetcherane+ ndi mbuye wanga mfumu ya Asuri,+ ndipo ine ndikupatsa mahatchi 2,000 kuti ndione ngati iweyo ungathe kupeza okwerapo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:8 Yesaya 1, ptsa. 386-387
8 Tsopano ubetcherane+ ndi mbuye wanga mfumu ya Asuri,+ ndipo ine ndikupatsa mahatchi 2,000 kuti ndione ngati iweyo ungathe kupeza okwerapo.+