-
Yesaya 36:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kodi ukuganiza kuti ndabwera kudzawononga dziko lino popanda chilolezo cha Yehova? Yehova weniweniyo wandiuza kuti, ‘Pita ukamenyane ndi dzikolo ndipo ukaliwononge.’”
-