Yesaya 36:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi ukuganiza kuti ndabwera kudzawononga dziko lino popanda chilolezo cha Yehova? Yehova weniweniyo wandiuza kuti,+ ‘Pita ukamenyane ndi dzikolo, ndipo ukaliwononge.’”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:10 Yesaya 1, ptsa. 386-387
10 Kodi ukuganiza kuti ndabwera kudzawononga dziko lino popanda chilolezo cha Yehova? Yehova weniweniyo wandiuza kuti,+ ‘Pita ukamenyane ndi dzikolo, ndipo ukaliwononge.’”+