Yesaya 36:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mfumuyo yanena kuti, ‘Musalole kuti Hezekiya akupusitseni, chifukwa sangathe kukupulumutsani.+