Yesaya 43:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwe sunandigulire bango lonunkhira* ndi ndalama zako,Ndipo sunandikhutitse ndi mafuta a nsembe zako.+ Mʼmalomwake, wanditopetsa ndi machimo akoNdipo wandilemetsa ndi zolakwa zako.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:24 Yesaya 2, ptsa. 57-59
24 Iwe sunandigulire bango lonunkhira* ndi ndalama zako,Ndipo sunandikhutitse ndi mafuta a nsembe zako.+ Mʼmalomwake, wanditopetsa ndi machimo akoNdipo wandilemetsa ndi zolakwa zako.+