Yesaya 50:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza.+ Nʼchifukwa chake sindidzamva kuti ndanyozeka. Nʼchifukwa chake ndalimbitsa nkhope yanga ngati mwala wa nsangalabwi,+Ndipo ndikudziwa kuti sindidzachititsidwa manyazi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 50:7 Yesaya 2, tsa. 161 Nsanja ya Olonda,8/1/1995, tsa. 15
7 Koma Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza.+ Nʼchifukwa chake sindidzamva kuti ndanyozeka. Nʼchifukwa chake ndalimbitsa nkhope yanga ngati mwala wa nsangalabwi,+Ndipo ndikudziwa kuti sindidzachititsidwa manyazi.