Yesaya 56:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, amene akusonkhanitsa pamodzi Aisiraeli omwe anabalalitsidwa,+ wanena kuti: “Ine ndidzamusonkhanitsira anthu ena kuwonjezera pa anthu ake amene anasonkhanitsidwa kale.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:8 Yesaya 2, tsa. 257
8 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, amene akusonkhanitsa pamodzi Aisiraeli omwe anabalalitsidwa,+ wanena kuti: “Ine ndidzamusonkhanitsira anthu ena kuwonjezera pa anthu ake amene anasonkhanitsidwa kale.”+