Yeremiya 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Nyumba yanga ndaisiya.+ Ndasiya cholowa changa.+ Wokondedwa wanga ndamupereka mʼmanja mwa adani ake.+
7 “Nyumba yanga ndaisiya.+ Ndasiya cholowa changa.+ Wokondedwa wanga ndamupereka mʼmanja mwa adani ake.+